[UAT #5] SMART Goal Bot

Smart Goal Bot for UAT

Consent

A bungwe la Dimagi akukuitanani kuti mutenge nawo gawo pa kafukufuku woyesa ma chatbots opangidwa kuti azithandizira alangizi azaumoyo. Tikukupemphani kuti:

Nthawi yoyembekezeredwa kuti mumalize ntchitoyi ikhala pafupifupi maola 5-6.

Kutenga nawo mbali ndi kosakakamizau, ndipo mutha kusankha kusiya kutenga nawo mbali nthawi iliyonse popanda chilango. Inu simulandira phindu lililonse potenga nawo mbali; komabe, mayankho anu angatithandize kuphunzira zambiri za momwe tingapangire bwino ma chatbots athu ndi maphunziro okhudzana a’mtsogolomu. Kutenga nawo mbali kuli ndi chiopsezo chokhudzana zachinsinsi zanu monga momwe munthu amagwiritsira ntchito intaneti tsiku ndi tsiku chifukwa nthawi zonse pamakhala chiopsezo chophwanya chinsinsichi. Komabe, tizayesesa kusamala kuti tichepese chiopsezo. Deta yosazindikirika yomwe yasonkhanitsidwa mu kafukufukuyu (i.e., mayankho a kafukufuku, kugwiritsa ntchito chatbot) iwunikidwa ndipo zotsatila zake zidzafotokozedwa mwachidule. Mayankho anu azipezeka ndi gulu la Dimagi lokha, ndipo deta yonse imene titatolele idzaoeneka mopanga chizindikiro chilichonse cha munthu. Deta idzasungidwa mu seva yotetezeka.

Ngati muli ndi mafunso kapena nkhawa zokhudzana ndi kutenga nawo gawo, chonde titumizireni uthenga wa email ku studies@dimagi.com.

Kusankha "I Agree" kumasonyeza kuti: